Kumanga Khola la M’mwamba la Nkhosa ndi mbuzi
Uploaded 3 years ago | Loading
08:52
M’makola ambiri, nkhosa kapena mbuzi zimakhala padothi. Ziwetozi zimagona mu mkodzo ndi ndowe zake. Chifukwa chosowa ukhondo, zambiri zimadwala.M’kanema uyu, tiwona momwe mungakonzere thandala loyika mu khola, kuti khola lanu likhale lam’mwamba.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Practical Action, Bangladesh and Nepal, Christian Commission for Development in Bangladesh (CCDB)