Misampha yogwira tintchentche tambiri muzipatso
Uploaded 1 year ago | Loading
13:00
Pheromone amakopa ndikupha tintchentche tatimuna, ndipo ssitingakumanenso ndi tintchentche tatikazi. Popanda kukumana ndiyekuti tintchentche tatikazi sitingaikire mazira. Kuti mukope ndikupha tintchentche tatimuna pogwiritsa ntchito Pheromone, muyenera kuika misampha yoteteza mankhwalawo kumvura. Misampha ina imapezeka ku sitolo koma muthanso kupanga yanu.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight