SLM08 Ntchito zankhalango
Uploaded 3 years ago | Loading
8:20
Reference book
Dzaka za mma 1970 nkhalangozi zinakumana ndi vuto la ng’amba:Mitengo yambiri inapululuka. Koma posachedwapa, Mvula yayamba kugwa kuphatikizapo khama la anthu komanso a mabungwe, nkhalango zozalidwa zabweleramo.Padzana, panali malingaliro ochepa pa zifukwa zomwe alimi amasamalira mitengo.Mwasiku ano anthu akutha kuyamikira kufunika kwa zinthu zachilngedwe ndinso phindu pachuma
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Countrywise Communication, CIS Vrije Universiteit Amsterdam