M’mene tingagwilisile ukonde wotetezela mbewu kuzilombo
Uploaded 7 years ago | Loading
11:35
Mbewa, nkhono ndi ziwala ndi zina mwazilombo zomwe zimawononga mbewu zathu. Mbewa zimakumba ndi kudya nthangala zomwe tangozala kumene. Nkhono zimadula mbande pamene zangotuluka. Ziwala nazo zimadula mbande za mbewu zathu. Pachifukwa cha ichi, timayenela kugwilitsa ntchito ukonde powonetsetsa kuti mbwewu zathu ndizotchinjilizidwa nthawi zonse.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight